-
Genesis 50:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu a Atadi mʼchigawo cha Yorodano. Kumeneko, anthuwo analira mokweza kwambiri, ndipo Yosefe analira maliro a bambo ake kwa masiku 7.
-