Mlaliki 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wosonkhanitsa anthu wanena kuti: “Nʼzachabechabe!Nʼzachabechabe! Zinthu zonse nʼzachabechabe!”+ Mlaliki 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,Ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe, zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
14 Ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,Ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe, zili ngati kuthamangitsa mphepo.+