1 Mafumu 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mulungu anapatsa Solomo nzeru, luso lozindikira komanso mtima womvetsa zinthu zambirimbiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.+ 1 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anapeka miyambi 3,000+ ndiponso nyimbo zokwana 1,005.+ Miyambo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Miyambi ya Solomo+ mwana wa Davide,+ mfumu ya Isiraeli:+
29 Mulungu anapatsa Solomo nzeru, luso lozindikira komanso mtima womvetsa zinthu zambirimbiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.+