1 Mafumu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Panatenga zaka 13 kuti Solomo amange nyumba* yake+ nʼkuimaliza.+