Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Aliyense amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,

      Munthu wopusa komanso munthu wopanda nzeru, onse amawonongeka,+

      Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+

  • Mlaliki 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,

      Ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe, zili ngati kuthamangitsa mphepo.+

  • Mlaliki 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa munthu wanzeru komanso munthu wopusa,+ onsewa sadzakumbukiridwa mpaka kalekale. Mʼmasiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalika. Ndipo kodi wanzeru adzafa bwanji? Adzafa mofanana ndi wopusa.+

  • 1 Timoteyo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pajatu sitinabwere ndi kanthu mʼdziko ndipo sitingachokemo ndi kanthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena