Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kukamuuza kuti: “Milungu yanga indilange mowirikiza, ngati pofika nthawi ino mawa sindidzakhala nditakupha ngati mmene waphera aneneriwo.”

  • 1 Mafumu 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndipo iyeyo analowa mʼchipululu nʼkuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Kenako anafika pa kamtengo kenakake nʼkukhala pansi pake. Ndiyeno anapempha kuti afe ponena kuti: “Basi ndatopa nazo. Tsopano chotsani moyo wanga Yehova,+ chifukwa siine woposa makolo anga.”

  • Yeremiya 20:17, 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Nʼchifukwa chiyani sanandiphe ndili mʼmimba,

      Kuti mayi anga akhale manda anga,

      Ndiponso kuti apitirize kukhala oyembekezera?+

      18 Nʼchifukwa chiyani ndinabadwa?

      Kodi ndinabadwa kuti ndidzaone mavuto komanso kukhala wachisoni,

      Kuti moyo wanga uthe mochititsa manyazi?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena