Mlaliki 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,Ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe, zili ngati kuthamangitsa mphepo.+ Mlaliki 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri:* Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Ndipo kodi munthu amene amagwira ntchito mwakhama koma zonse nʼkungopita ndi mphepo amapindula chiyani?+
14 Ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,Ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe, zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri:* Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Ndipo kodi munthu amene amagwira ntchito mwakhama koma zonse nʼkungopita ndi mphepo amapindula chiyani?+