Mlaliki 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi munthu amapeza chiyani pa ntchito yake yonse yovutaImene amaigwira mwakhama padziko lapansi pano?*+ Mlaliki 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi munthu wogwira ntchito amapeza phindu lanji pa ntchito yonse imene akugwira mwakhama?+
3 Kodi munthu amapeza chiyani pa ntchito yake yonse yovutaImene amaigwira mwakhama padziko lapansi pano?*+