Mlaliki 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu otuluka mʼkamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamubweretsera mavuto.+
12 Mawu otuluka mʼkamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamubweretsera mavuto.+