Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anali ndi ziweto zambiri ndipo anaona kuti dera la Yazeri+ komanso la Giliyadi, anali malo abwino a ziweto.

  • Deuteronomo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawi imeneyo tinatenga dzikoli kukhala lathu kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼchigwa cha Arinoni* ndi hafu ya dera lamapiri la Giliyadi. Ndipo ndinapereka mizinda yake kwa fuko la Rubeni ndi fuko la Gadi.+

  • Nyimbo ya Solomo 6:5-7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yangʼana kumbali kuti maso ako+ asandiyangʼanitsitse,

      Chifukwa akundichititsa mantha.

      Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuzi

      Zimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+

       6 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa

      Zimene zikuchokera kosambitsidwa,

      Zonse zabereka mapasa,

      Ndipo palibe imene ana ake afa.

       7 Masaya ako munsalu yako yophimba kumutuyo

      Ali ngati khangaza* logamphula pakati.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena