Nyimbo ya Solomo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Undikise ndi milomo yako,Chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo.+ Nyimbo ya Solomo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nditenge, tiye tithawe. Chifukwatu mfumu yandipititsa mʼzipinda zake zamkati. Tiye tikondwere komanso kusangalalira limodzi. Tiye titamande* chikondi chimene umandisonyeza kuposa kutamanda vinyo. Mpake kuti atsikana amakukonda.
4 Nditenge, tiye tithawe. Chifukwatu mfumu yandipititsa mʼzipinda zake zamkati. Tiye tikondwere komanso kusangalalira limodzi. Tiye titamande* chikondi chimene umandisonyeza kuposa kutamanda vinyo. Mpake kuti atsikana amakukonda.