Miyambo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+