Yesaya 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Deralo lidzachitadi maluwa.+Lidzasangalala ndipo lidzafuula chifukwa cha chisangalalo. Lidzapatsidwa ulemerero wa Lebanoni,+Kukongola kwa Karimeli+ ndiponso kwa Sharoni.+ Anthu adzaona ulemerero wa Yehova ndi kukongola kwa Mulungu wathu.
2 Deralo lidzachitadi maluwa.+Lidzasangalala ndipo lidzafuula chifukwa cha chisangalalo. Lidzapatsidwa ulemerero wa Lebanoni,+Kukongola kwa Karimeli+ ndiponso kwa Sharoni.+ Anthu adzaona ulemerero wa Yehova ndi kukongola kwa Mulungu wathu.