Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pali munthu amene ntchito yake ndi yogwetsa mitengo ya mkungudza.

      Iye amasankha mtengo wamtundu winawake, mtengo waukulu kwambiri,

      Ndipo amausiya kuti ukule nʼkukhwima pakati pa mitengo yamʼnkhalango.+

      Iye amadzala mtengo wa paini ndipo mvula imaukulitsa.

      15 Kenako mtengowo umakhala nkhuni zoti munthu akolezere moto.

      Amatenga mbali ina ya mtengowo kuti asonkhere moto woti aziwotha.

      Amayatsa moto nʼkuphikapo mkate.

      Koma amasemanso mulungu nʼkumamulambira.

      Mtengowo amaupanga chifaniziro chosema ndipo amachigwadira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena