Salimo 121:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Amene akuyangʼanira Isiraeli,+Sadzawodzera kapena kugona. Yesaya 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine Yehova ndikulondera mkaziyo.+ Ndimamuthirira nthawi zonse.+ Ndimamulondera masana ndi usiku,Kuti wina aliyense asamuvulaze.+
3 Ine Yehova ndikulondera mkaziyo.+ Ndimamuthirira nthawi zonse.+ Ndimamulondera masana ndi usiku,Kuti wina aliyense asamuvulaze.+