Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani. Amosi 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubweraPamene ndidzatumiza njala mʼdziko.Osati njala ya chakudya kapena ludzu lofuna madzi,Koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.+
48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani.
11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubweraPamene ndidzatumiza njala mʼdziko.Osati njala ya chakudya kapena ludzu lofuna madzi,Koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.+