Yesaya 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amuna ako adzaphedwa ndi lupanga,Ndipo amuna ako amphamvu adzaphedwa pa nkhondo.+