Yeremiya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+
16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+