-
Zekariya 2:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu anthu azidzakhalamo+ ngati mzinda wopanda mpanda chifukwa cha anthu onse ndiponso ziweto zimene zili mmenemo.+ 5 Ine ndidzakhala ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ulemerero wanga udzadzaza mumzindawu,”’+ watero Yehova.”
-