-
Yesaya 25:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chifukwa inu mwakhala malo otetezeka kwa munthu wonyozeka
Malo otetezeka kwa munthu wosauka pamene akukumana ndi mavuto.+
Mwakhala malo obisalirapo mvula yamkuntho
Ndiponso mthunzi wobisalirapo kutentha kwa dzuwa.+
Mwakhala wotero pamene anthu ankhanza akuwomba anzawo ngati mvula yamkuntho imene ikuwomba khoma.
-