Yeremiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi vuto lotani+Kuti asochere nʼkupita kutali ndi ine,Nʼkuyamba kutsatira mafano opanda pake,+ iwonso nʼkukhala anthu opanda pake?+ Hoseya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kunyada kwa Aisiraeli kwakhala umboni wowatsutsa,+Koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+Ndiponso sanamufunefune ngakhale kuti pali zonsezi. Mika 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu anthu anga, ndakulakwirani chiyani? Kodi ndachita chiyani kuti ndikutopetseni?+ Perekani umboni wonditsutsa.
5 Yehova wanena kuti: “Kodi makolo anu anandipeza ndi vuto lotani+Kuti asochere nʼkupita kutali ndi ine,Nʼkuyamba kutsatira mafano opanda pake,+ iwonso nʼkukhala anthu opanda pake?+
10 Kunyada kwa Aisiraeli kwakhala umboni wowatsutsa,+Koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+Ndiponso sanamufunefune ngakhale kuti pali zonsezi.
3 “Inu anthu anga, ndakulakwirani chiyani? Kodi ndachita chiyani kuti ndikutopetseni?+ Perekani umboni wonditsutsa.