-
Yesaya 1:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndikudana ndi zikondwerero zimene mumachita mwezi watsopano ukaoneka komanso zikondwerero zina.
Zimenezi zasanduka katundu wolemera kwa ine,
Ndatopa ndi kuzinyamula.
-