Ezekieli 34:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa adzalandira madalitso+ ndipo ndidzachititsa kuti mvula igwe pa nthawi yake. Madalitso adzagwa ambiri ngati mvula.+
26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa adzalandira madalitso+ ndipo ndidzachititsa kuti mvula igwe pa nthawi yake. Madalitso adzagwa ambiri ngati mvula.+