16 Ndinu osokoneza zinthu kwambiri!
Kodi woumba zinthu ndi dongo angafanane ndi dongolo?+
Kodi chinthu chimene chinapangidwa, chinganene za amene anachipanga kuti:
“Iye uja sanandipange”?+
Komanso kodi chinthu chochita kuumbidwa chinganene za amene anachiumba kuti:
“Iye uja samvetsa zinthu”?+