Yesaya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide.