Yesaya 43:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine Yehova.+ Palibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.”+ Yesaya 60:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwe udzamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+Ndipo udzayamwa bere la mafumu.+Udzadziwadi kuti ine Yehova ndine Mpulumutsi wako,Ndiponso kuti Wamphamvu wa Yakobo ndi Wokuwombola.+ Tito 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma pa nthawi yake, anachititsa kuti mawu ake adziwike kudzera mu ntchito yolalikira imene ndinapatsidwa+ mogwirizana ndi lamulo la Mpulumutsi wathu, Mulungu.
16 Iwe udzamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+Ndipo udzayamwa bere la mafumu.+Udzadziwadi kuti ine Yehova ndine Mpulumutsi wako,Ndiponso kuti Wamphamvu wa Yakobo ndi Wokuwombola.+
3 Koma pa nthawi yake, anachititsa kuti mawu ake adziwike kudzera mu ntchito yolalikira imene ndinapatsidwa+ mogwirizana ndi lamulo la Mpulumutsi wathu, Mulungu.