Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+
9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+