Yesaya 45:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sonkhanani pamodzi ndipo mubwere. Mubwere pamodzi, inu anthu amene mwapulumuka ku mitundu ya anthu.+ Amene amanyamula zifaniziro zawo zogoba sadziwa chilichonseNdipo amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+
20 Sonkhanani pamodzi ndipo mubwere. Mubwere pamodzi, inu anthu amene mwapulumuka ku mitundu ya anthu.+ Amene amanyamula zifaniziro zawo zogoba sadziwa chilichonseNdipo amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+