Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 137:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+

      Wosangalala adzakhala amene adzakubwezere

      Zimene iwe watichitira.+

  • Yeremiya 50:41, 42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto.

      Mtundu wamphamvu ndi mafumu akuluakulu+ adzakonzekera kuukira

      Kuchokera kumadera akutali kwambiri a dziko lapansi.+

      42 Iwo amadziwa kuponya mivi ndi uta komanso nthungo.+

      Amenewo ndi anthu ankhanza ndipo sadzakumvera chifundo.+

      Phokoso lawo lili ngati phokoso la nyanja imene ikuchita mafunde.+

      Amachita phokosoli akakwera pamahatchi.

      Mogwirizana, iwo ayalana pokonzekera kumenyana nawe, iwe mwana wamkazi wa Babulo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena