Yeremiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa a mʼnyumba ya Isiraeli ndi a mʼnyumba ya YudaAndichitira zachinyengo kwambiri,” akutero Yehova.+ Yeremiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikanakonda ndikanakhala ndi malo ogona anthu apaulendo mʼchipululu. Zikanatero, ndikanasiya anthu a mtundu wanga nʼkuwachokera,Chifukwa onse ndi achigololo,+Gulu la anthu ochita zachinyengo.
11 Chifukwa a mʼnyumba ya Isiraeli ndi a mʼnyumba ya YudaAndichitira zachinyengo kwambiri,” akutero Yehova.+
2 Ndikanakonda ndikanakhala ndi malo ogona anthu apaulendo mʼchipululu. Zikanatero, ndikanasiya anthu a mtundu wanga nʼkuwachokera,Chifukwa onse ndi achigololo,+Gulu la anthu ochita zachinyengo.