Yesaya 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakupatsani chilango,Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+ Yeremiya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba akuti: “Ine ndidzawayenga komanso kuwayesa,+Nanga mwana wamkazi wa anthu anga ndingamuchitirenso chiyani?
25 Ndidzakupatsani chilango,Ndidzakuyengani nʼkuchotseratu zonyansa zanu zonse,Ndidzachotsa zinthu zonse zimene zikuchititsa kuti musakhale oyera.+
7 Choncho, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba akuti: “Ine ndidzawayenga komanso kuwayesa,+Nanga mwana wamkazi wa anthu anga ndingamuchitirenso chiyani?