Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Chivumbulutso 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova* Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera, Wamphamvuyonse.”+ Chivumbulutso 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndine Alefa ndi Omega,*+ woyamba ndi wotsiriza, chiyambi ndi mapeto.
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+
8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova* Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera, Wamphamvuyonse.”+