Amosi 5:23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Siyani kuimba nyimbo zaphokoso,Ndipo sindikufuna kumva nyimbo zanu zoimbidwa ndi zoimbira za zingwe.+ 24 Chilungamo chiyende ngati madzi.+Ndiponso ngati mtsinje wosaphwa nthawi zonse.
23 Siyani kuimba nyimbo zaphokoso,Ndipo sindikufuna kumva nyimbo zanu zoimbidwa ndi zoimbira za zingwe.+ 24 Chilungamo chiyende ngati madzi.+Ndiponso ngati mtsinje wosaphwa nthawi zonse.