-
Ekisodo 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Anapatsa munthu pakamwa ndi ndani, kapena ndi ndani amene ali ndi mphamvu zopangitsa munthu kukhala wosalankhula, wogontha, woona kapena wosaona? Kodi si ine, Yehova?
-