Yohane 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ayudawo anadabwa nʼkufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu Malemba+ amenewa anawadziwa* bwanji, popeza sanapite kusukulu?”*+ Yohane 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Alondawo anayankha kuti: “Palibe munthu amene analankhulapo ngati iyeyu nʼkale lonse.”+
15 Ayudawo anadabwa nʼkufunsa kuti: “Kodi munthu ameneyu Malemba+ amenewa anawadziwa* bwanji, popeza sanapite kusukulu?”*+