-
Ezekieli 3:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma ndachititsa kuti nkhope yako ikhale yolimba mofanana ndi nkhope zawo, ndiponso chipumi chako kuti chikhale cholimba mofanana ndi zipumi zawo.+ 9 Ndachititsa kuti chipumi chako chikhale ngati mwala wa dayamondi, cholimba kuposa mwala wa nsangalabwi.+ Usawaope kapena kuchita mantha ndi nkhope zawo,+ chifukwa iwo ndi anthu opanduka.”
-