Chivumbulutso 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼmalo opatulikawo munadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa mʼmalo opatulikawo mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.
8 Mʼmalo opatulikawo munadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa mʼmalo opatulikawo mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.