Yakobo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yandikirani Mulungu ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu+ okayikakayika inu.
8 Yandikirani Mulungu ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu+ okayikakayika inu.