Yesaya 61:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa ine Yehova ndimakonda chilungamo.+Ndimadana ndi zauchifwamba komanso zinthu zopanda chilungamo.+ Anthu anga ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,Ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+
8 Chifukwa ine Yehova ndimakonda chilungamo.+Ndimadana ndi zauchifwamba komanso zinthu zopanda chilungamo.+ Anthu anga ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,Ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+