Chivumbulutso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+ Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene Ame+ akunena, yemwe ndi mboni+ yokhulupirika komanso yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+
14 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene Ame+ akunena, yemwe ndi mboni+ yokhulupirika komanso yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+