Ezekieli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ngati munthu woipa wasiya kuchita machimo ake onse amene ankachita ndipo akusunga malamulo anga nʼkumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, ndithu iye adzapitiriza kukhala ndi moyo. Sadzafa ayi.+ Machitidwe 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa zibwere kuchokera kwa Yehova.*
21 Koma ngati munthu woipa wasiya kuchita machimo ake onse amene ankachita ndipo akusunga malamulo anga nʼkumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, ndithu iye adzapitiriza kukhala ndi moyo. Sadzafa ayi.+
19 Choncho lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa zibwere kuchokera kwa Yehova.*