Salimo 103:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mofanana ndi mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,Chikondi chokhulupirika chimene amasonyeza anthu amene amamuopa ndi chachikulu kwambiri.+
11 Mofanana ndi mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,Chikondi chokhulupirika chimene amasonyeza anthu amene amamuopa ndi chachikulu kwambiri.+