Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 49:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Taona! Ineyo ndidzakwezera dzanja langa mitundu ya anthu,

      Ndipo anthu a mitundu ina ndidzawakwezera chizindikiro.+

      Iwo adzakubweretsera ana ako aamuna atawanyamula mʼmanja,*

      Ndipo ana ako aakazi adzawanyamula paphewa.+

  • Yesaya 60:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Kweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira.

      Onse asonkhanitsidwa pamodzi. Akubwera kwa iwe.

      Ana ako aamuna akubwerabe kuchokera kutali,+

      Ndipo ana ako aakazi akubwera atanyamulidwa mʼmanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena