13 “Chifukwa aliyense kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, akupeza phindu mwachinyengo.+
Kuyambira mneneri mpaka wansembe, aliyense akuchita zachinyengo.+
14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti,
‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’