Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mukawonongeretu malo onse amene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo,+ kaya ndi pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.

  • 1 Mafumu 14:22, 23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ayuda ankachita zoipa pamaso pa Yehova+ ndipo anamukwiyitsa kwambiri ndi machimo awo kuposa mmene makolo awo anachitira.+ 23 Nawonso anapitiriza kumanga malo okwezeka, zipilala zopatulika ndi mizati yopatulika*+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wamasamba obiriwira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena