Yeremiya 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi awo akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘Mfumukazi Yakumwamba.’*+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+
18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi awo akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘Mfumukazi Yakumwamba.’*+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+