Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Unamanga malo ako okwerawo pamalo oonekera bwino kwambiri mumsewu uliwonse ndipo kukongola kwako unakusandutsa chinthu chonyansa podzipereka kwa munthu* aliyense wodutsa+ ndipo unachulukitsa zochita zako zauhulezo.+

  • Ezekieli 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Anthu amapereka mphatso kwa mahule onse,+ koma iweyo ndi amene wapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa ziphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+

  • Ezekieli 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Oholiba atapitiriza kuchita uhule mopanda manyazi komanso kudzivula,+ ine ndinamusiya chifukwa chonyansidwa naye, ngati mmene ndinasiyira mchemwali wake chifukwa chonyansidwa naye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena