Salimo 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Utachita zinthu zimenezi, ine sindinalankhule kanthu,Choncho unkaganiza kuti ndikuona zinthu ngati mmene iweyo ukuzionera. Koma tsopano ndikudzudzulaNdipo ndikuuza mlandu umene ndakupeza nawo.+
21 Utachita zinthu zimenezi, ine sindinalankhule kanthu,Choncho unkaganiza kuti ndikuona zinthu ngati mmene iweyo ukuzionera. Koma tsopano ndikudzudzulaNdipo ndikuuza mlandu umene ndakupeza nawo.+