Yobu 34:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akakwiyira anthu,Nʼkutenga mphamvu ya moyo* komanso mpweya wawo,+15 Anthu onse amafera limodzi,Ndipo anthuwo amabwerera kufumbi.+
14 Iye akakwiyira anthu,Nʼkutenga mphamvu ya moyo* komanso mpweya wawo,+15 Anthu onse amafera limodzi,Ndipo anthuwo amabwerera kufumbi.+