Ezekieli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma a nyumba ya Isiraeli akakana kukumvera, chifukwa iwo sakufuna kundimvera.+ Anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani komanso osamva.+
7 Koma a nyumba ya Isiraeli akakana kukumvera, chifukwa iwo sakufuna kundimvera.+ Anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani komanso osamva.+